-
Yesaya 57:1, 2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
57 Wolungama wawonongedwa,
Koma palibe amene zikumukhudza.
2 Iye amalowa mumtendere.
Onse amene amayenda mowongoka amapita kukapuma mʼmanda.*
-