-
Miyambo 22:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Usabere munthu wosauka chifukwa choti ndi wosauka,+
Ndipo usapondereze munthu wonyozeka pageti la mzinda,+
-
Amosi 5:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Chifukwa ndikudziwa kuchuluka kwa zochita zanu zondigalukira,
Ndiponso kukula kwa machimo anu.
Mumachitira nkhanza munthu wolungama,
Mumalandira ziphuphu,
Komanso mumaphwanya ufulu wa anthu osauka pageti la mzinda.+
-
-
-