Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Yobu 7:6, 7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Masiku anga akuthamanga kuposa mashini owombera nsalu,+

      Atha mofulumira ndipo ine ndilibe chiyembekezo.+

       7 Kumbukirani kuti moyo wanga uli ngati mphepo,+

      Ndiponso kuti diso langa silidzaonanso zinthu zosangalatsa.*

  • Salimo 103:15, 16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Masiku a moyo wa munthu ali ngati masiku a udzu.+

      Iye amaphuka ngati duwa lakutchire.+

      16 Koma mphepo ikawomba limafa,

      Ndipo zimangokhala ngati panalibepo.*

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani