-
Yobu 24:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Osaukawo amafunafuna chakudya ngati abulu+ amʼchipululu,
Amafunafuna chakudya cha ana awo mʼchipululu.
-
-
Salimo 104:10, 11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Amatulutsa madzi mu akasupe kuti apite mʼzigwa*
Ndipo madziwo amadutsa pakati pa mapiri.
11 Akasupewo amapereka madzi kwa zilombo zonse zakutchire.
Abulu amʼtchire amapha ludzu lawo mmenemo.
-