Maliro 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ngakhale mimbulu imapereka bere kwa ana ake kuti ayamwe,Koma mwana wamkazi wa anthu anga wakhala wankhanza+ ngati nthiwatiwa zamʼchipululu.+
3 Ngakhale mimbulu imapereka bere kwa ana ake kuti ayamwe,Koma mwana wamkazi wa anthu anga wakhala wankhanza+ ngati nthiwatiwa zamʼchipululu.+