Salimo 147:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Iye sachita chidwi ndi mphamvu za hatchi,+Kapena miyendo ya munthu yomwe ndi yamphamvu.+ Yesaya 31:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Tsoka kwa anthu amene amapita ku Iguputo kukapempha thandizo,+Amene amadalira mahatchi,+Amene amadalira magaleta ankhondo chifukwa chakuti ndi ambiri,Komanso mahatchi ankhondo* chifukwa chakuti ndi amphamvu kwambiri. Koma sayangʼana kwa Woyera wa Isiraeli,Ndipo safunafuna Yehova.
31 Tsoka kwa anthu amene amapita ku Iguputo kukapempha thandizo,+Amene amadalira mahatchi,+Amene amadalira magaleta ankhondo chifukwa chakuti ndi ambiri,Komanso mahatchi ankhondo* chifukwa chakuti ndi amphamvu kwambiri. Koma sayangʼana kwa Woyera wa Isiraeli,Ndipo safunafuna Yehova.