Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Yesaya 5:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Mivi yawo ndi yakuthwa,

      Ndipo mauta awo onse ndi okungika.*

      Ziboda za mahatchi awo nʼzolimba ngati mwala wa nsangalabwi,

      Ndipo mawilo a magaleta awo ali ngati mphepo yamkuntho.+

  • Yeremiya 8:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Ine ndinatchera khutu ndipo ndinapitiriza kuwamvetsera. Koma zimene iwo ankanena sizinali zoona.

      Panalibe munthu amene analapa zoipa zimene ankachita, kapena amene anafunsa kuti, ‘Nʼchiyani chimene ndachitachi?’+

      Aliyense akungobwerera kunjira imene anthu ambiri akuitsatira, ngati hatchi imene ikuthamangira kunkhondo.

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani