-
Yobu 1:14, 15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 kunabwera munthu kwa Yobu kudzanena uthenga wakuti: “Ngʼombe zimalima ndipo abulu amadya msipu chapambali pake. 15 Kenako Asabeya anabwera nʼkutiukira ndipo analanda ziweto nʼkupha atumiki anu ndi lupanga. Ine ndekha ndi amene ndapulumuka, choncho ndabwera kudzakuuzani uthengawu.”
-