Yobu 14:5, 6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Masiku a munthu ndi odziwika,Ndipo chiwerengero cha miyezi yake chili mʼmanja mwanu.Mwamuikira malire kuti asapitirire.+ 6 Siyani kumuyangʼanitsitsa kuti apume,Mpaka atamaliza tsiku lake ngati mmene amachitira waganyu.+ Salimo 39:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
5 Masiku a munthu ndi odziwika,Ndipo chiwerengero cha miyezi yake chili mʼmanja mwanu.Mwamuikira malire kuti asapitirire.+ 6 Siyani kumuyangʼanitsitsa kuti apume,Mpaka atamaliza tsiku lake ngati mmene amachitira waganyu.+