-
Mlaliki 3:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Ine ndaonanso zinthu izi padziko lapansi pano: Pamene panayenera kukhala chilungamo panali zoipa, ndipo pamene panayenera kuchitika zachilungamo panachitika zoipa.+
-