-
1 Samueli 19:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Nthawi yomweyo, Mikala anathandiza Davide kuti atulukire pawindo nʼkuthawa.
-
-
Salimo 18:48Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
48 Iye amandipulumutsa kwa adani anga olusa.
Mumandikweza pamwamba pa anthu amene amandiukira.+
Mumandipulumutsa kwa munthu wachiwawa.
-
-
Salimo 71:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Inu Mulungu wanga, ndipulumutseni mʼmanja mwa woipa,+
Kuti ndisagwidwe ndi munthu wochita zinthu mopondereza komanso wopanda chilungamo.
-