Salimo 37:12, 13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Munthu woipa amakonzera chiwembu munthu wolungama,+Ndipo amamukukutira mano. 13 Koma Yehova adzamuseka,Chifukwa akudziwa kuti mapeto ake adzafika.+
12 Munthu woipa amakonzera chiwembu munthu wolungama,+Ndipo amamukukutira mano. 13 Koma Yehova adzamuseka,Chifukwa akudziwa kuti mapeto ake adzafika.+