-
Salimo 21:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Dzanja lanu lidzapeza adani anu onse.
Dzanja lanu lamanja lidzapeza anthu amene amadana nanu.
-
-
Salimo 108:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Kuti anthu amene mumawakonda apulumutsidwe,
Tipulumutseni ndi dzanja lanu lamanja ndipo mundiyankhe.+
-