Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Yoswa 13:29-31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Komanso Mose anapereka cholowa kwa hafu ya fuko la Manase motsatira mabanja awo.+ 30 Dera lawo linayambira ku Mahanaimu,+ dera lonse la Basana, dziko lonse limene linali kulamulidwa ndi Mfumu Ogi ya Basana ndiponso midzi yonse yaingʼono ya Yairi+ ku Basana. Dera lawoli linali ndi matauni 60. 31 Mose anapereka hafu ya dera la Giliyadi, Asitaroti, Edirei+ ndi mizinda ya ufumu wa Ogi mʼdziko la Basana kwa ana a Makiri,+ mwana wa Manase. Anapereka dzikoli kwa hafu ya ana a Makiri motsatira mabanja awo.

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani