-
Salimo 68:2, 3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Mofanana ndi mphepo imene imathamangitsa utsi, inunso muwathamangitsire kutali.
Mofanana ndi phula limene limasungunuka pamoto,
Anthu oipa awonongeke pamaso pa Mulungu.+
-