Salimo 63:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Salimo 109:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Koma inu, Yehova Ambuye Wamkulu Koposa,Ndithandizeni kuti dzina lanu lilemekezedwe.+ Ndipulumutseni chifukwa chikondi chanu chokhulupirika nʼchabwino.+
21 Koma inu, Yehova Ambuye Wamkulu Koposa,Ndithandizeni kuti dzina lanu lilemekezedwe.+ Ndipulumutseni chifukwa chikondi chanu chokhulupirika nʼchabwino.+