Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Salimo 10:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Koma inu Yehova mudzamva pempho la anthu ofatsa.+

      Mudzalimbitsa mitima yawo+ ndipo mudzawamvetsera mwatcheru.+

  • Salimo 102:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Adzamvetsera pemphero la anthu osauka.+

      Iye sadzapeputsa pemphero lawo.+

  • Yesaya 66:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 “Dzanja langa ndi limene linapanga zinthu zonsezi,

      Ndipo izi ndi zimene zinachitika kuti zonsezi zikhalepo,” akutero Yehova.+

      “Choncho ine ndidzayangʼana munthu ameneyu,

      Ndidzayangʼana munthu wodzichepetsa ndiponso wosweka mtima amene amadera nkhawa mawu anga.+

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani