-
Salimo 25:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
Musalole kuti adani anga asangalale chifukwa cha mavuto anga.+
-
-
Yeremiya 17:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Anthu amene amandizunza achite manyazi,+
Koma musalole kuti ineyo ndichite manyazi.
Anthuwo agwidwe ndi mantha aakulu,
Koma musalole kuti ine ndigwidwe ndi mantha aakulu.
-