2 Samueli 22:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Davide analankhula ndi Yehova mawu a nyimbo iyi,+ pa tsiku limene Yehova anamupulumutsa kwa adani ake onse+ ndiponso mʼmanja mwa Sauli.+ 1 Mbiri 16:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kenako Davide anaika Alevi ena kuti azitumikira kumene Likasa la Yehova+ linkakhala ndiponso kuti azilemekeza,* kuyamika komanso kutamanda Yehova Mulungu wa Isiraeli. Salimo 9:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
22 Davide analankhula ndi Yehova mawu a nyimbo iyi,+ pa tsiku limene Yehova anamupulumutsa kwa adani ake onse+ ndiponso mʼmanja mwa Sauli.+
4 Kenako Davide anaika Alevi ena kuti azitumikira kumene Likasa la Yehova+ linkakhala ndiponso kuti azilemekeza,* kuyamika komanso kutamanda Yehova Mulungu wa Isiraeli.