-
Salimo 46:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Pali mtsinje umene nthambi zake zimachititsa kuti anthu amumzinda wa Mulungu asangalale,+
Chihema chachikulu chopatulika cha Wamʼmwambamwamba.
-