Salimo 50:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Amene akundiyamikira kuti ikhale nsembe imene akupereka kwa ine akundilemekeza.+Ndipo munthu amene akupitiriza kuchita zabwino,Ndidzamuonetsa chipulumutso changa.”+ Salimo 100:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Lowani pamageti ake mukumuyamikira,+Lowani mʼmabwalo ake mukumutamanda.+ Muyamikeni, tamandani dzina lake.+
23 Amene akundiyamikira kuti ikhale nsembe imene akupereka kwa ine akundilemekeza.+Ndipo munthu amene akupitiriza kuchita zabwino,Ndidzamuonetsa chipulumutso changa.”+
4 Lowani pamageti ake mukumuyamikira,+Lowani mʼmabwalo ake mukumutamanda.+ Muyamikeni, tamandani dzina lake.+