-
Amosi 9:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Akadzabisala pamwamba pa phiri la Karimeli,
Ndidzawafufuza mosamala nʼkuwatenga,+
Ndipo akadzathawa pamaso panga nʼkubisala pansi pa nyanja,
Ndidzalamula njoka kuti iwalume pomwepo.
-