2 Mbiri 9:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Zinali choncho chifukwa zombo za mfumu zinkapita ku Tarisi+ limodzi ndi atumiki a Hiramu.+ Kamodzi pa zaka zitatu zilizonse, zombozo zinkabweretsa golide, siliva, minyanga ya njovu,+ anyani ndi mbalame zotchedwa pikoko. Ezekieli 27:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Amuna odziwa ntchito* komanso aluso a ku Gebala+ ndi amene ankamata molumikizira matabwa ako.+ Sitima zonse zapanyanja ndi anthu amene ankaziyendetsa ankabwera kwa iwe kudzagulitsa malonda.
21 Zinali choncho chifukwa zombo za mfumu zinkapita ku Tarisi+ limodzi ndi atumiki a Hiramu.+ Kamodzi pa zaka zitatu zilizonse, zombozo zinkabweretsa golide, siliva, minyanga ya njovu,+ anyani ndi mbalame zotchedwa pikoko.
9 Amuna odziwa ntchito* komanso aluso a ku Gebala+ ndi amene ankamata molumikizira matabwa ako.+ Sitima zonse zapanyanja ndi anthu amene ankaziyendetsa ankabwera kwa iwe kudzagulitsa malonda.