-
1 Mafumu 17:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Koma patapita masiku angapo,+ mtsinjewo unauma chifukwa mʼdzikomo simunkagwa mvula.
-
-
Yesaya 42:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Ndidzawononga mapiri ndi zitunda
Ndi kuumitsa zomera zonse zimene zili mmenemo.
-