Yesaya 45:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Mbadwa* zonse za Isiraeli zidzaona kuti zinachita bwino kutumikira Yehova,+Ndipo zidzadzitama chifukwa cha zinthu zimene iye anazichitira.’”
25 Mbadwa* zonse za Isiraeli zidzaona kuti zinachita bwino kutumikira Yehova,+Ndipo zidzadzitama chifukwa cha zinthu zimene iye anazichitira.’”