1 Mbiri 10:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Salimo 53:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma adzagwidwa ndi mantha aakulu,Mantha amene sanayambe agwidwapo chiyambire,*Chifukwa Mulungu adzamwaza mafupa a anthu amene akukuukirani.* Mudzawachititsa manyazi chifukwa Yehova wawakana. Yesaya 59:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Njira ya mtendere sakuidziwa,Ndipo mʼnjira zawo mulibe chilungamo.+ Misewu yawo aikhotetsakhotetsa.Palibe munthu aliyense woyenda mmenemo amene adzadziwe mtendere.+
5 Koma adzagwidwa ndi mantha aakulu,Mantha amene sanayambe agwidwapo chiyambire,*Chifukwa Mulungu adzamwaza mafupa a anthu amene akukuukirani.* Mudzawachititsa manyazi chifukwa Yehova wawakana.
8 Njira ya mtendere sakuidziwa,Ndipo mʼnjira zawo mulibe chilungamo.+ Misewu yawo aikhotetsakhotetsa.Palibe munthu aliyense woyenda mmenemo amene adzadziwe mtendere.+