Yeremiya 51:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Iwe mkazi amene ukukhala pamadzi ambiri,+Amene uli ndi chuma chambiri,+Mapeto ako afika ndipo nthawi yako yopanga phindu yatha.+ Ezekieli 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Choncho ndinapita kwa anthu amene anatengedwa kupita ku ukapolo omwe anali ku Tele-abibu. Anthuwa ankakhala pafupi ndi mtsinje wa Kebara.+ Ndinakhala nawo kumeneko masiku 7 nditasokonezeka maganizo.+ Danieli 10:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pa tsiku la 24 la mwezi woyamba, ndili mʼmbali mwa mtsinje waukulu, mtsinje wa Tigirisi,*+
13 “Iwe mkazi amene ukukhala pamadzi ambiri,+Amene uli ndi chuma chambiri,+Mapeto ako afika ndipo nthawi yako yopanga phindu yatha.+
15 Choncho ndinapita kwa anthu amene anatengedwa kupita ku ukapolo omwe anali ku Tele-abibu. Anthuwa ankakhala pafupi ndi mtsinje wa Kebara.+ Ndinakhala nawo kumeneko masiku 7 nditasokonezeka maganizo.+