Yobu 10:10, 11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kodi simunandikhuthule ngati mkakaNʼkundichititsa kuti ndiundane ngati tchizi?* 11 Munandiveka khungu ndiponso mnofu,Ndipo munandiluka ndi mafupa komanso mitsempha.+
10 Kodi simunandikhuthule ngati mkakaNʼkundichititsa kuti ndiundane ngati tchizi?* 11 Munandiveka khungu ndiponso mnofu,Ndipo munandiluka ndi mafupa komanso mitsempha.+