-
Salimo 36:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Musalole kuti phazi la anthu odzikweza lindipondereze
Kapena kuti dzanja la anthu oipa lindithamangitse.
-
-
Salimo 71:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Inu Mulungu wanga, ndipulumutseni mʼmanja mwa woipa,+
Kuti ndisagwidwe ndi munthu wochita zinthu mopondereza komanso wopanda chilungamo.
-