Salimo 62:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iwo amakambirana kuti amuchotse pa udindo wake wapamwamba.*Bodza limawasangalatsa. Iwo amadalitsa ndi pakamwa pawo, koma mumtima mwawo amakhala akutemberera.+ (Selah)
4 Iwo amakambirana kuti amuchotse pa udindo wake wapamwamba.*Bodza limawasangalatsa. Iwo amadalitsa ndi pakamwa pawo, koma mumtima mwawo amakhala akutemberera.+ (Selah)