2 Samueli 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Davide anadziwa kuti Yehova wachititsa kuti ufumu wake ukhazikike mu Isiraeli,+ komanso kuti ukhale wamphamvu+ chifukwa cha anthu a Mulungu, Aisiraeli.+ Salimo 89:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
12 Davide anadziwa kuti Yehova wachititsa kuti ufumu wake ukhazikike mu Isiraeli,+ komanso kuti ukhale wamphamvu+ chifukwa cha anthu a Mulungu, Aisiraeli.+