-
Yeremiya 11:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Ndinali ngati mwana wa nkhosa wamphongo womvera amene akupita kukaphedwa.
Sindinadziwe kuti andikonzera chiwembu nʼkunena kuti:+
“Tiyeni tiwononge mtengowu limodzi ndi zipatso zake,
Ndipo tiyeni timuchotse mʼdziko la anthu amoyo,
Kuti dzina lake lisadzakumbukiridwenso.”
-