Rute 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Zitatero, Boazi anapita kugeti la mzinda+ nʼkukhala pansi. Ali kumeneko anaona wowombola anamutchula uja+ akudutsa. Ndiyeno Boazi anati: “Iwe uje, tabwera udzakhale apa.” Choncho anapita nʼkukakhala pansi. Yobu 29:7, 8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
4 Zitatero, Boazi anapita kugeti la mzinda+ nʼkukhala pansi. Ali kumeneko anaona wowombola anamutchula uja+ akudutsa. Ndiyeno Boazi anati: “Iwe uje, tabwera udzakhale apa.” Choncho anapita nʼkukakhala pansi.