Levitiko 19:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Usamayendeyende pakati pa anthu a mtundu wako nʼkumafalitsa miseche.+ Usachite kanthu kalikonse kuti uphetse mnzako.*+ Ine ndine Yehova. Agalatiya 5:20, 21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Yakobo 3:14, 15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
16 Usamayendeyende pakati pa anthu a mtundu wako nʼkumafalitsa miseche.+ Usachite kanthu kalikonse kuti uphetse mnzako.*+ Ine ndine Yehova.