-
Miyambo 26:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
26 Sinowo sayenera kugwa mʼchilimwe ndiponso mvula siyenera kugwa pa nthawi yokolola,
Chimodzimodzinso munthu wopusa, iye sayenera kulemekezedwa.+
-