-
Miyambo 19:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Ulesi umabweretsa tulo tofa nato,
Ndipo munthu waulesi adzakhala ndi njala.+
-
-
Miyambo 24:33, 34Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
33 Ukapitiriza kugona pangʼono, ukapitiriza katulo pangʼono,
Ukapitiriza kupinda manja pangʼono kuti upume,
34 Umphawi wako udzabwera ngati wachifwamba,
Ndipo kusauka kwako kudzabwera ngati munthu wokhala ndi zida.+
-