-
Esitere 7:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Choncho Hamani anamupachika pamtengo umene anakonzera Moredikayi, ndipo mkwiyo wa mfumu unatha.
-
-
Salimo 9:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Mitundu ya anthu yagwera mʼdzenje limene anakumba okha.
Phazi lawo lakodwa mu ukonde umene anatchera okha.+
-
-
Mlaliki 10:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Amene akukumba dzenje angathe kugweramo+ ndipo amene akugumula mpanda wamiyala angathe kulumidwa ndi njoka.
-