-
Zefaniya 3:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Akalonga ake ali ngati mikango yobangula.+
Oweruza ake ali ngati mimbulu imene ikuyenda usiku.
Imene pofika mʼmawa imadya chilichonse osasiya ngakhale fupa.
-