-
Deuteronomo 17:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 mudzasankhe mfumu imene Yehova Mulungu wanu adzasankhe.+ Mudzasankhe mfumuyo kuchokera pakati pa abale anu. Simukuloledwa kusankha mlendo amene si mʼbale wanu.
-