-
Yeremiya 20:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Nʼchifukwa chiyani ndinabadwa?
Kodi ndinabadwa kuti ndidzaone mavuto komanso kukhala wachisoni,
Kuti moyo wanga uthe mochititsa manyazi?+
-