-
Yesaya 43:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Chifukwa ine ndine Yehova Mulungu wako,
Woyera wa Isiraeli, Mpulumutsi wako.
Ndapereka Iguputo kuti akhale dipo* lako.
Ndaperekanso Itiyopiya ndi Seba mʼmalo mwa iwe.
-