Yesaya 48:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Bwerani pafupi ndi ine ndipo mumve izi. Kuyambira pachiyambi, ine sindinalankhulirepo mʼmalo obisika.+ Kuyambira pamene zinachitika ine ndinalipo.” Ndipo panopa Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, watumiza ine komanso* mzimu wake.
16 Bwerani pafupi ndi ine ndipo mumve izi. Kuyambira pachiyambi, ine sindinalankhulirepo mʼmalo obisika.+ Kuyambira pamene zinachitika ine ndinalipo.” Ndipo panopa Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, watumiza ine komanso* mzimu wake.