Yesaya 45:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Koma Isiraeli adzapulumutsidwa ndi Yehova ndipo chipulumutso chake chidzakhala chosatha.+ Inu simudzachititsidwa manyazi kapena kunyozeka mpaka kalekale.+ Luka 1:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
17 Koma Isiraeli adzapulumutsidwa ndi Yehova ndipo chipulumutso chake chidzakhala chosatha.+ Inu simudzachititsidwa manyazi kapena kunyozeka mpaka kalekale.+