Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Yesaya 65:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Yesaya 66:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Ndi ndani anamvapo zinthu ngati zimenezi?

      Ndi ndani anaonapo zinthu zoterezi?

      Kodi dziko lingabadwe tsiku limodzi?

      Kapena kodi mtundu wa anthu ungabadwe nthawi imodzi?

      Koma Ziyoni atangoyamba kumva zowawa za pobereka, anabereka ana aamuna.

  • Yesaya 66:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 “Chifukwa kumwamba kwatsopano ndi dziko lapansi latsopano+ zimene ndikupanga zidzapitiriza kukhala pamaso panga. Mofanana ndi zimenezi, ana anu* ndi dzina lanu zidzapitiriza kukhalapo,”+ akutero Yehova.

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani