Yesaya 52:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 Dzuka! Dzuka! Vala mphamvu+ iwe Ziyoni.+ Vala zovala zako zokongola+ iwe Yerusalemu, mzinda woyera. Chifukwa munthu wosadulidwa ndi wodetsedwa sadzabweranso mwa iwe.+ Yesaya 60:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 60 “Imirira mkazi iwe!+ Onetsa kuwala kwako, chifukwa kuwala kwako kwafika. Ulemerero wa Yehova wakuunikira.+
52 Dzuka! Dzuka! Vala mphamvu+ iwe Ziyoni.+ Vala zovala zako zokongola+ iwe Yerusalemu, mzinda woyera. Chifukwa munthu wosadulidwa ndi wodetsedwa sadzabweranso mwa iwe.+
60 “Imirira mkazi iwe!+ Onetsa kuwala kwako, chifukwa kuwala kwako kwafika. Ulemerero wa Yehova wakuunikira.+