-
2 Mafumu 16:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Pa nthawiyi mʼpamene Rezini mfumu ya Siriya ndi Peka mwana wa Remaliya mfumu ya Isiraeli, anapita kukamenyana ndi anthu amumzinda wa Yerusalemu.+ Anazungulira mzindawu, womwe Ahazi ankakhala, koma sanathe kuulanda.
-