Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • 2 Mafumu 15:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Kenako Hoshiya+ mwana wa Ela anakonzera chiwembu Peka mwana wa Remaliya nʼkumupha. Atatero anakhala mfumu mʼmalo mwake mʼchaka cha 20 cha Yotamu+ mwana wa Uziya.

  • Yesaya 8:6, 7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 “Popeza anthu awa akana madzi a ku Silowa*+ amene amayenda pangʼonopangʼono,

      Ndipo akusangalala ndi Rezini ndiponso mwana wa Remaliya,+

       7 Yehova adzawabweretsera

      madzi ambiri komanso amphamvu a mu Mtsinje*

      Omwe ndi mfumu ya Asuri+ ndi ulemerero wake wonse.

      Mfumuyo idzadzaza timitsinje take tonse

      Nʼkusefukira mʼmphepete mwake monse

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani