-
Yeremiya 25:32, 33Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
32 Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti:
‘Taonani! Tsoka likufalikira kuchokera ku mtundu wina kupita ku mtundu wina,+
Ndipo mkuntho wamphamvu udzafika kuchokera kumadera akutali kwambiri a dziko lapansi.+
33 Pa tsiku limenelo anthu amene adzaphedwe ndi Yehova adzachokera kumalekezero a dziko lapansi kukafika kumalekezero ena a dziko lapansi. Maliro awo sadzaliridwa, sadzawasonkhanitsa pamodzi kapena kuwaika mʼmanda. Iwo adzakhala ngati manyowa panthaka.’
-