Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Salimo 86:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Mitundu yonse ya anthu imene munapanga

      Idzabwera nʼkudzagwada pamaso panu, inu Yehova,+

      Ndipo idzalemekeza dzina lanu.+

  • Zekariya 14:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Aliyense wotsala mwa anthu a mitundu yonse obwera kudzamenyana ndi Yerusalemu, chaka chilichonse+ azidzapita kukagwadira* Mfumu, Yehova wa magulu ankhondo akumwamba,+ ndiponso kukachita nawo Zikondwerero za Misasa.+

  • Malaki 1:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 “Kuchokera kotulukira dzuwa kukafika kumene limalowera,* dzina langa lidzakwezeka pakati pa anthu a mitundu ina.+ Kulikonse anthu azidzapereka nsembe zautsi ndiponso nsembe zina ngati mphatso zovomerezeka polemekeza dzina langa. Adzachita izi chifukwa dzina langa lidzakwezeka pakati pa anthu a mitundu inawo,”+ watero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani