-
Yeremiya 4:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Kwezani chizindikiro choloza njira ya ku Ziyoni.
Thawirani kumalo otetezeka, musangoima,”
Chifukwa ndikubweretsa tsoka kuchokera kumpoto,+ tsoka lalikulu kwambiri.
-